M’bowo
Kim Joo-Young
Editorial: Bookey
Sinopsis
Mabowo mu zovala za Mikie zikusonyeza umphawi. Mikie amabisala muchire mmalo moptia kusukulu chifukwa amachita manyazi ndi zovala zake zobooka Ulendo wa Mikie unayamba pamene iye mokhumundwaanagwera mu bowo pomwe amaliyang\' anitsita.